-
Aheberi 13:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 akupatseni zinthu zonse zofunika kuti muchite chifuniro chake. Ndipo kudzera mwa Yesu Khristu, atithandize kuchita zinthu zomusangalatsa. Mulungu alandire ulemerero mpaka kalekale. Ame.
-