Yakobo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 kodi mumasangalala ndi amene wavala zovala zapamwamba uja nʼkumuuza kuti, “Khalani pamalo abwinowa” koma wosauka uja nʼkumuuza kuti: “Iwe ubaima choncho,” kapena, “Khala pansipa pafupi ndi chopondapo mapazi anga”?+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:3 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, ptsa. 13-14
3 kodi mumasangalala ndi amene wavala zovala zapamwamba uja nʼkumuuza kuti, “Khalani pamalo abwinowa” koma wosauka uja nʼkumuuza kuti: “Iwe ubaima choncho,” kapena, “Khala pansipa pafupi ndi chopondapo mapazi anga”?+