Yakobo 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako anapempheranso ndipo mvula inagwa kuchokera kumwamba moti nthaka inatulutsa zipatso zake.+