1 Petulo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene mukubwera kwa Ambuye, amene ndi mwala wamoyo umene anthu anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso ndi wamtengo wapatali kwa Mulunguyo,+
4 Pamene mukubwera kwa Ambuye, amene ndi mwala wamoyo umene anthu anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso ndi wamtengo wapatali kwa Mulunguyo,+