-
2 Petulo 1:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pa chifukwa chimenechi, ndikufuna kuti ndizikukumbutsani zinthu zimenezi nthawi zonse, ngakhale kuti mukuzidziwa kale ndipo ndinu olimba mʼchoonadi chimene munaphunzira.
-