2 Petulo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 koma anadzudzulidwa chifukwa cholephera kuchita zinthu zabwino.+ Bulu amene salankhula, analankhula ngati munthu nʼkulepheretsa zochita zamisala za mneneriyo.+ 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 17
16 koma anadzudzulidwa chifukwa cholephera kuchita zinthu zabwino.+ Bulu amene salankhula, analankhula ngati munthu nʼkulepheretsa zochita zamisala za mneneriyo.+