-
2 Petulo 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Iye anafotokoza zimenezi ngati mmene amachitira mʼmakalata ake onse. Komabe mʼmakalata akewo muli zinthu zina zovuta kuzimvetsa, zimene anthu osaphunzitsika komanso achikhulupiriro chosalimba akuzipotoza. Amachita zimenezi ngati mmene amachitiranso ndi Malemba ena onse, zomwe zidzachititse kuti adzawonongedwe.
-