1 Yohane 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo amatsanzira Mdyerekezi, chifukwa Mdyerekezi wakhala akuchimwa kuyambira pachiyambi.*+ Nʼchifukwa chake Mwana wa Mulungu anaonekera kuti awononge ntchito za Mdyerekezi.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:8 Nsanja ya Olonda,4/15/1999, ptsa. 11-127/1/1998, tsa. 122/1/1987, tsa. 9
8 Amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo amatsanzira Mdyerekezi, chifukwa Mdyerekezi wakhala akuchimwa kuyambira pachiyambi.*+ Nʼchifukwa chake Mwana wa Mulungu anaonekera kuti awononge ntchito za Mdyerekezi.+