1 Yohane 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuti tidziwe ngati mawu ouziridwa ndi ochokera kwa Mulungu, timadziwira izi: Mawu alionse ouziridwa amene amavomereza zoti Yesu Khristu anabwera monga munthu ndi ochokera kwa Mulungu.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:2 Nsanja ya Olonda,2/1/1987, ptsa. 12-13
2 Kuti tidziwe ngati mawu ouziridwa ndi ochokera kwa Mulungu, timadziwira izi: Mawu alionse ouziridwa amene amavomereza zoti Yesu Khristu anabwera monga munthu ndi ochokera kwa Mulungu.+