1 Yohane 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nʼchifukwa chake ife tikusonyeza chikondi mokwanira kuti tidzathe kulankhula momasuka+ pa tsiku lachiweruzo, chifukwa mmene Yesu Khristu alili, ndi mmenenso ife tilili mʼdzikoli. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:17 Nsanja ya Olonda,2/1/1987, tsa. 15
17 Nʼchifukwa chake ife tikusonyeza chikondi mokwanira kuti tidzathe kulankhula momasuka+ pa tsiku lachiweruzo, chifukwa mmene Yesu Khristu alili, ndi mmenenso ife tilili mʼdzikoli.