-
3 Yohane 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Anthu onse akhala akumuchitira umboni Demetiriyo. Komanso zochita zake zogwirizana ndi choonadi zimamuchitira umboni. Ifenso tikumuchitira umboni, ndipo ukudziwa kuti umboni umene timapereka ndi woona.
-