Chivumbulutso 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 18-19 Nsanja ya Olonda,12/1/1999, tsa. 10
5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+