Chivumbulutso 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 nʼkutipanga kukhala mafumu+ ndi ansembe+ kuti titumikire Mulungu wake ndi Atate wake, kwa iyeyo kukhale ulemerero ndi mphamvu kwamuyaya. Ame. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 19
6 nʼkutipanga kukhala mafumu+ ndi ansembe+ kuti titumikire Mulungu wake ndi Atate wake, kwa iyeyo kukhale ulemerero ndi mphamvu kwamuyaya. Ame.