Chivumbulutso 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera ngati ubweya woyera wa nkhosa, zinali zoyera kwambiri, ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:14 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 25
14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera ngati ubweya woyera wa nkhosa, zinali zoyera kwambiri, ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+