Chivumbulutso 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale zili choncho, uli ndi anthu angapo* mu Sade amene sanadetse zovala zawo+ ndipo adzayenda ndi ine atavala zovala zoyera,+ chifukwa ndi oyenerera. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:4 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 56-58 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 17
4 Ngakhale zili choncho, uli ndi anthu angapo* mu Sade amene sanadetse zovala zawo+ ndipo adzayenda ndi ine atavala zovala zoyera,+ chifukwa ndi oyenerera.