Chivumbulutso 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ‘Ndikudziwa ntchito zako. Taona! Ndatsegula khomo pamaso pako+ limene wina sangalitseke. Ndikudziwa kuti uli ndi mphamvu zochepa ndiponso kuti unasunga mawu anga. Ndikudziwanso kuti wakhala wokhulupirika ku dzina langa. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:8 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 60-61, 62-65 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 174/1/1989, tsa. 12
8 ‘Ndikudziwa ntchito zako. Taona! Ndatsegula khomo pamaso pako+ limene wina sangalitseke. Ndikudziwa kuti uli ndi mphamvu zochepa ndiponso kuti unasunga mawu anga. Ndikudziwanso kuti wakhala wokhulupirika ku dzina langa.