-
Chivumbulutso 3:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 ‘Ndikudziwa ntchito zako, kuti si iwe wozizira kapena wotentha. Ndikanakonda ukanakhala wozizira kapena wotentha.
-