-
Chivumbulutso 4:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Zimenezi zitatha, ndinayangʼana kumwamba ndipo ndinaona khomo lotseguka. Mawu oyamba amene ndinamva akundilankhula anali ngati kulira kwa lipenga. Mawuwo anali akuti: “Kwera kumwamba kuno ndipo ndikuonetsa zinthu zimene zikuyenera kuchitika.”
-