Chivumbulutso 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako nthawi yomweyo mzimu wa Mulungu unayamba kugwira ntchito mwa ine ndipo mpando wachifumu unaoneka uli pamalo ake kumwamba, wina atakhalapo.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:2 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 74-76
2 Kenako nthawi yomweyo mzimu wa Mulungu unayamba kugwira ntchito mwa ine ndipo mpando wachifumu unaoneka uli pamalo ake kumwamba, wina atakhalapo.+