Chivumbulutso 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuzungulira mpando wachifumuwo panalinso mipando yachifumu yokwana 24. Pamipando yachifumuyo, ndinaona patakhala akulu 24+ atavala zovala zoyera komanso zisoti zachifumu zagolide kumutu kwawo. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:4 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 76-77, 102-103, 288-289 Nsanja ya Olonda,7/1/1995, tsa. 13
4 Kuzungulira mpando wachifumuwo panalinso mipando yachifumu yokwana 24. Pamipando yachifumuyo, ndinaona patakhala akulu 24+ atavala zovala zoyera komanso zisoti zachifumu zagolide kumutu kwawo.