Chivumbulutso 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ndinaona mpukutu umene unalembedwa mbali zonse,* uli mʼdzanja lamanja la Mulungu amene anakhala pampando wachifumu.+ Mpukutuwo anaumata molimba ndi zidindo 7 zomatira. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 82-83
5 Kenako ndinaona mpukutu umene unalembedwa mbali zonse,* uli mʼdzanja lamanja la Mulungu amene anakhala pampando wachifumu.+ Mpukutuwo anaumata molimba ndi zidindo 7 zomatira.