-
Chivumbulutso 5:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma panalibe aliyense kaya kumwamba, padziko lapansi kapena pansi pa nthaka, amene anatha kutsegula mpukutuwo kapena kuyangʼanamo ndi kuuwerenga.
-