Chivumbulutso 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma mmodzi wa akulu aja anandiuza kuti: “Tonthola. Taona! Mkango wa fuko la Yuda,+ muzu+ wa Davide,+ anapambana pankhondo+ moti ndi woyenera kumatula zidindo 7 zimene amatira mpukutuwo nʼkuutsegula.” Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:5 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 35-36 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 83-84 Nsanja ya Olonda,8/15/1994, tsa. 31
5 Koma mmodzi wa akulu aja anandiuza kuti: “Tonthola. Taona! Mkango wa fuko la Yuda,+ muzu+ wa Davide,+ anapambana pankhondo+ moti ndi woyenera kumatula zidindo 7 zimene amatira mpukutuwo nʼkuutsegula.”
5:5 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 35-36 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 83-84 Nsanja ya Olonda,8/15/1994, tsa. 31