Chivumbulutso 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzombelo silinaloledwe kupha anthuwo, koma linauzidwa kuti liwazunze kwa miyezi 5. Ndipo kuzunzika kwawo kunali kofanana ndi mmene munthu amazunzikira akalumidwa ndi chinkhanira.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:5 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 144-145, 147-148 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, ptsa. 12-13
5 Dzombelo silinaloledwe kupha anthuwo, koma linauzidwa kuti liwazunze kwa miyezi 5. Ndipo kuzunzika kwawo kunali kofanana ndi mmene munthu amazunzikira akalumidwa ndi chinkhanira.+