Chivumbulutso 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dzombelo linkaoneka ngati mahatchi okonzekera nkhondo.+ Pamitu pawo panali zinthu zooneka ngati zisoti zachifumu zagolide. Nkhope zawo zinali ngati nkhope za anthu, Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 145-146, 153
7 Dzombelo linkaoneka ngati mahatchi okonzekera nkhondo.+ Pamitu pawo panali zinthu zooneka ngati zisoti zachifumu zagolide. Nkhope zawo zinali ngati nkhope za anthu,