Chivumbulutso 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dzombelo lili ndi mfumu yomwe ndi mngelo wa phompho.+ MʼChiheberi dzina lake ndi Abadoni,* koma mʼChigiriki ali ndi dzina lakuti Apoliyoni.* Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:11 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 143, 148
11 Dzombelo lili ndi mfumu yomwe ndi mngelo wa phompho.+ MʼChiheberi dzina lake ndi Abadoni,* koma mʼChigiriki ali ndi dzina lakuti Apoliyoni.*