Chivumbulutso 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Masiku oti mngelo wa 7+ alize lipenga akadzatsala pangʼono kukwana,+ chinsinsi chopatulika+ chimene Mulungu analengeza kwa akapolo ake aneneri,+ monga uthenga wabwino, chidzakwaniritsidwa ndithu.” Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 157-158, 171-172 Nsanja ya Olonda,1/15/1990, ptsa. 19-204/1/1989, tsa. 1912/15/1988, ptsa. 13-14
7 Masiku oti mngelo wa 7+ alize lipenga akadzatsala pangʼono kukwana,+ chinsinsi chopatulika+ chimene Mulungu analengeza kwa akapolo ake aneneri,+ monga uthenga wabwino, chidzakwaniritsidwa ndithu.”
10:7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 157-158, 171-172 Nsanja ya Olonda,1/15/1990, ptsa. 19-204/1/1989, tsa. 1912/15/1988, ptsa. 13-14