-
Chivumbulutso 11:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ngati wina aliyense akufuna kuzivulaza, moto umatuluka mʼkamwa mwawo nʼkupsereza adani awo. Ngati wina angafune kuzivulaza, ayenera kuphedwa mwanjira imeneyi.
-