-
Chivumbulutso 11:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mitembo yawo idzagona pamsewu waukulu wamumzinda waukulu, umene mophiphiritsa ukutchedwa Sodomu ndi Iguputo, kumenenso Ambuye wawo anaphedwa powapachika pamtengo.
-