-
Chivumbulutso 11:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Amene akukhala padziko lapansi adzasangalala ndi kukondwera chifukwa cha imfa yawoyo. Iwo adzatumizirana mphatso chifukwa aneneri awiriwa anazunza amene akukhala padziko lapansi.
-