-
Chivumbulutso 11:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mu ola limenelo, kunachitika chivomerezi chachikulu ndipo gawo limodzi mwa magawo 10 a mzindawo linagwa. Anthu 7,000 anaphedwa ndi chivomerezicho ndipo ena onse anachita mantha nʼkupereka ulemerero kwa Mulungu wakumwamba.
-