Chivumbulutso 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chilombocho chinapatsidwa pakamwa polankhula zinthu zodzitukumula ndi zonyoza Mulungu. Chinapatsidwanso mphamvu yochita zimene chikufuna kwa miyezi 42.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:5 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 192
5 Chilombocho chinapatsidwa pakamwa polankhula zinthu zodzitukumula ndi zonyoza Mulungu. Chinapatsidwanso mphamvu yochita zimene chikufuna kwa miyezi 42.+