Chivumbulutso 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mngelo woyamba anapita nʼkukathira mbale yake padziko lapansi.+ Atatero, anthu amene anali ndi chizindikiro cha chilombo+ komanso amene ankalambira chifaniziro chake,+ anagwidwa ndi mliri wa zilonda zopweteka+ komanso zoopsa. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:2 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 221-223
2 Mngelo woyamba anapita nʼkukathira mbale yake padziko lapansi.+ Atatero, anthu amene anali ndi chizindikiro cha chilombo+ komanso amene ankalambira chifaniziro chake,+ anagwidwa ndi mliri wa zilonda zopweteka+ komanso zoopsa.