Chivumbulutso 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mngelo wa 5 anathira mbale yake pampando wachifumu wa chilombo. Ufumu wa chilombocho unachita mdima+ ndipo anthu anayamba kudziluma malilime chifukwa cha ululu. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:10 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 227-228
10 Mngelo wa 5 anathira mbale yake pampando wachifumu wa chilombo. Ufumu wa chilombocho unachita mdima+ ndipo anthu anayamba kudziluma malilime chifukwa cha ululu.