Chivumbulutso 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anafuula ndi mawu amphamvu akuti: “Wagwa! Babulo Wamkulu wagwa,+ ndipo wakhala malo amene ziwanda zimakhala. Wakhalanso malo amene mzimu uliwonse wonyansa* komanso mbalame iliyonse yonyansa ndi imene imadedwa zimabisala.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:2 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 58 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 259-261 Nsanja ya Olonda,5/1/1989, ptsa. 3-54/15/1989, tsa. 9
2 Iye anafuula ndi mawu amphamvu akuti: “Wagwa! Babulo Wamkulu wagwa,+ ndipo wakhala malo amene ziwanda zimakhala. Wakhalanso malo amene mzimu uliwonse wonyansa* komanso mbalame iliyonse yonyansa ndi imene imadedwa zimabisala.+
18:2 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 58 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 259-261 Nsanja ya Olonda,5/1/1989, ptsa. 3-54/15/1989, tsa. 9