Chivumbulutso 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa muyezo umene anadzipezera ulemerero ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, pa muyezo womwewo mumuzunze ndi kumuliritsa. Chifukwa mumtima mwake akumanena kuti: ‘Ine ndine mfumukazi. Si ine mkazi wamasiye ndipo sindidzalira.’+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266 Yesaya 2, tsa. 119
7 Pa muyezo umene anadzipezera ulemerero ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, pa muyezo womwewo mumuzunze ndi kumuliritsa. Chifukwa mumtima mwake akumanena kuti: ‘Ine ndine mfumukazi. Si ine mkazi wamasiye ndipo sindidzalira.’+