Chivumbulutso 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mafumu a dziko lapansi amene anachita naye chiwerewere* nʼkumasangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa pomumvera chisoni, akadzaona utsi ukufuka chifukwa cha kupsa kwake. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:9 Nsanja ya Olonda,2/15/2009, tsa. 5 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 267
9 Mafumu a dziko lapansi amene anachita naye chiwerewere* nʼkumasangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa pomumvera chisoni, akadzaona utsi ukufuka chifukwa cha kupsa kwake.