Chivumbulutso 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo adzaima patali chifukwa cha mantha poona mmene akuzunzikira ndipo adzanena kuti: ‘Zomvetsa chisoni! Zomvetsa chisoni! Iwe mzinda waukulu,+ iwe Babulo mzinda wamphamvu! Chifukwa mu ola limodzi lokha, chiweruzo chako chafika!’ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:10 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 267
10 Iwo adzaima patali chifukwa cha mantha poona mmene akuzunzikira ndipo adzanena kuti: ‘Zomvetsa chisoni! Zomvetsa chisoni! Iwe mzinda waukulu,+ iwe Babulo mzinda wamphamvu! Chifukwa mu ola limodzi lokha, chiweruzo chako chafika!’