-
Chivumbulutso 18:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Katundu wawoyo ndi golide, siliva, miyala yamtengo wapatali, ngale, nsalu zabwino kwambiri, nsalu zapepo, nsalu zasilika ndi nsalu zofiira kwambiri. Palibe amene akuwagula chilichonse chopangidwa kuchokera ku mtengo wa fungo labwino, zinthu zosiyanasiyana zopangidwa ndi minyanga, mtengo wapamwamba, kopa, chitsulo ndi mwala wa mabo.
-