Chivumbulutso 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso palibe amene akuwagula sinamoni, zonunkhiritsa zochokera ku Indiya, zofukiza, mafuta onunkhira, lubani, vinyo, mafuta a maolivi, ufa wabwino kwambiri, tirigu, ngʼombe, nkhosa, mahatchi, ngolo, akapolo ndiponso anthu ena.* Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:13 Nsanja ya Olonda,1/1/2009, tsa. 23 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 267-268
13 Komanso palibe amene akuwagula sinamoni, zonunkhiritsa zochokera ku Indiya, zofukiza, mafuta onunkhira, lubani, vinyo, mafuta a maolivi, ufa wabwino kwambiri, tirigu, ngʼombe, nkhosa, mahatchi, ngolo, akapolo ndiponso anthu ena.*