Chivumbulutso 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kuwala kwa nyale sikudzaunikanso mwa iwe. Mawu a mkwati ndi a mkwatibwi sadzamvekanso mwa iwe, chifukwa amalonda ako anali anthu apamwamba padziko lapansi, ndiponso mitundu yonse ya anthu inasocheretsedwa ndi zochita zako zamizimu.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:23 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 269-270 Nsanja ya Olonda,5/1/1989, ptsa. 6-74/1/1989, tsa. 4
23 Kuwala kwa nyale sikudzaunikanso mwa iwe. Mawu a mkwati ndi a mkwatibwi sadzamvekanso mwa iwe, chifukwa amalonda ako anali anthu apamwamba padziko lapansi, ndiponso mitundu yonse ya anthu inasocheretsedwa ndi zochita zako zamizimu.+