Chivumbulutso 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi chiwerewere* chake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”*+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:2 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 272 Nsanja ya Olonda,4/15/1989, tsa. 16
2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi chiwerewere* chake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”*+