Chivumbulutso 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiye akulu 24+ ndi angelo 4 aja,+ anagwada pansi nʼkuwerama ndipo analambira Mulungu amene wakhala pampando wachifumu, nʼkunena kuti: “Ame! Tamandani Ya!”*+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:4 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 273-274
4 Ndiye akulu 24+ ndi angelo 4 aja,+ anagwada pansi nʼkuwerama ndipo analambira Mulungu amene wakhala pampando wachifumu, nʼkunena kuti: “Ame! Tamandani Ya!”*+