Chivumbulutso 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Amene anakwera pahatchiyo dzina lake linali lakuti Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iye amaweruza molungama ndipo akumenya nkhondo mwachilungamo.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, tsa. 17 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 280
11 Ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Amene anakwera pahatchiyo dzina lake linali lakuti Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iye amaweruza molungama ndipo akumenya nkhondo mwachilungamo.+