Chivumbulutso 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu zambiri. Iye analembedwa dzina limene palibe wina aliyense amene akulidziwa koma iye yekha. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:12 Nsanja ya Olonda,2/15/2009, tsa. 5 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 65, 280-281
12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu zambiri. Iye analembedwa dzina limene palibe wina aliyense amene akulidziwa koma iye yekha.