Chivumbulutso 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 kuti mudzadye minofu ya mafumu, ya akuluakulu a asilikali, ya amuna amphamvu,+ ya mahatchi ndi ya amene akwera pamahatchiwo,+ minofu ya onse, ya mfulu ndi ya akapolo, ya olemekezeka ndi ya onyozeka.” Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:18 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 13, 284-285
18 kuti mudzadye minofu ya mafumu, ya akuluakulu a asilikali, ya amuna amphamvu,+ ya mahatchi ndi ya amene akwera pamahatchiwo,+ minofu ya onse, ya mfulu ndi ya akapolo, ya olemekezeka ndi ya onyozeka.”