Chivumbulutso 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma ena onse anaphedwa ndi lupanga lalitali limene linkatuluka mʼkamwa mwa amene anakwera pahatchi+ uja. Ndipo mbalame zonse zinakhuta minofu yawo.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:21 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 285-286
21 Koma ena onse anaphedwa ndi lupanga lalitali limene linkatuluka mʼkamwa mwa amene anakwera pahatchi+ uja. Ndipo mbalame zonse zinakhuta minofu yawo.+