-
Chivumbulutso 21:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Aliyense amene wapambana pankhondo adzalandira zinthu zimenezi kuti zikhale cholowa chake. Ineyo ndidzakhala Mulungu wake ndipo iye adzakhala mwana wanga.
-