Chivumbulutso 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho, pogwiritsa ntchito mphamvu ya mzimu, ananditenga nʼkundipititsa kuphiri lalikulu ndi lalitali ndipo anandionetsa mzinda woyera wa Yerusalemu, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu,+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:10 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 305-306
10 Choncho, pogwiritsa ntchito mphamvu ya mzimu, ananditenga nʼkundipititsa kuphiri lalikulu ndi lalitali ndipo anandionetsa mzinda woyera wa Yerusalemu, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu,+