Chivumbulutso 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno amene ankandilankhula uja ananyamula bango lagolide loyezera, kuti ayeze mzindawo, mageti ake ndi mpanda wake.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:15 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 306
15 Ndiyeno amene ankandilankhula uja ananyamula bango lagolide loyezera, kuti ayeze mzindawo, mageti ake ndi mpanda wake.+